Constitution of Zimbabwe 2013 (PDF Format) CHEWA

NOTE by Veritas
This is a translation of the original 2013 text of the Constitution of Zimbabwe.
It does not include amendments made by Acts of Parliament in 2017 and 2021;
the validity of those Acts is still the subject of litigation in the Constitutional Court.
 

LAMULO
Kuchotsa ndi kuyikanso Lamulo lalikulu la Zimbabwe.
ZOPANGIDWA ndi Mtsogoleli wa dziko ndi Nyumba yaMalamulo yaZimbabwe.
1 Mutu mwachidule
Lamulo lalikuluili likhoza kuchulidwa Lamulo lalikulu la Zimbabwe Lokonzedwa Mwatsopano (No. 20) 2013.
2 Kumasulila
MuLamulo limeneli—
“Lamulo Lalikululi limene likugwira ntchito” kutanthauza Lamulo lalikulu la Zimbabwe limene linayamba kugwila ntchito pa tsiku la 18th April, 1980, mongalinga ndi momwe linakonzedwela;
“Lamulo lalikulu la Zimbabwe” kutanthauza Lamulo lalikulu la Zimbabwe limene lomwe lili mu dongosolo lachinayi.

 

Download File 🔗 

Tags